Kugwiritsa Ntchito Moyenera Masamba Amchezo

Kugwiritsa Ntchito Moyenera Masamba Amchezo

Bungwe la Centre for Multiparty Democracy (CMD) lapempha achinyamata kuti azigwiritsa ntchito moyenera masamba amchezo osati kunyoza kapena kubweretsa chisokonezo mdziko pomwe dziko lino lichititse chisankho posachedwapa Malinga ndi m’modzi wa oyendetsa ntchito ku CMD...
CMD